Luka 7:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Pamenepo onse amene anakhala naye patebulopo anayamba kudzifunsa mumtima mwawo kuti: “Kodi munthu ameneyu n’ngotani wokhozanso ngakhale kukhululukira machimo?”+
49 Pamenepo onse amene anakhala naye patebulopo anayamba kudzifunsa mumtima mwawo kuti: “Kodi munthu ameneyu n’ngotani wokhozanso ngakhale kukhululukira machimo?”+