Luka 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho ngati Satana wagawanika, ufumu wake ungalimbe bwanji?+ Chifukwa inu mukuti ndikutulutsa ziwanda ndi mphamvu ya Belezebule.
18 Choncho ngati Satana wagawanika, ufumu wake ungalimbe bwanji?+ Chifukwa inu mukuti ndikutulutsa ziwanda ndi mphamvu ya Belezebule.