Luka 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako umapita kukatenga mizimu ina 7+ yoipa kwambiri kuposa umenewu, ndipo ikalowa mkatimo, imakhala mmenemo. Potsirizira pake zochita za munthu ameneyu zimakhala zoipa kwambiri kuposa poyamba paja.”+
26 Kenako umapita kukatenga mizimu ina 7+ yoipa kwambiri kuposa umenewu, ndipo ikalowa mkatimo, imakhala mmenemo. Potsirizira pake zochita za munthu ameneyu zimakhala zoipa kwambiri kuposa poyamba paja.”+