Luka 11:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho ngati thupi lako lonse lili lowala kwambiri, popanda mbali ina yamdima, thupi lonse lidzawala kwambiri+ ngati mmene nyale imachitira pokuunikira ndi kuwala kwake.”
36 Choncho ngati thupi lako lonse lili lowala kwambiri, popanda mbali ina yamdima, thupi lonse lidzawala kwambiri+ ngati mmene nyale imachitira pokuunikira ndi kuwala kwake.”