Luka 11:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Pa nkhani imeneyi, nzeru+ ya Mulungu inanenanso kuti, ‘Ndidzawatumizira aneneri ndi atumwi, koma iwo adzapha ndi kuzunza ena mwa iwo.
49 Pa nkhani imeneyi, nzeru+ ya Mulungu inanenanso kuti, ‘Ndidzawatumizira aneneri ndi atumwi, koma iwo adzapha ndi kuzunza ena mwa iwo.