Luka 12:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Gulitsani+ zinthu zanu ndi kupereka mphatso zachifundo.+ Dzipangireni zikwama za ndalama zomwe sizingathe, kutanthauza chuma chosatha kumwamba,+ kumene mbala singafikeko, ndipo njenjete* singawononge. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:33 Yesu—Ndi Njira, tsa. 181 Nsanja ya Olonda,10/1/1988, tsa. 8
33 Gulitsani+ zinthu zanu ndi kupereka mphatso zachifundo.+ Dzipangireni zikwama za ndalama zomwe sizingathe, kutanthauza chuma chosatha kumwamba,+ kumene mbala singafikeko, ndipo njenjete* singawononge.