Luka 12:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Pa nthawiyo kapolo amene anadziwa zofuna za mbuye wake koma osakonzekera kubwera kwake, kapena osachita mogwirizana ndi zofuna za mbuye wakeyo, adzakwapulidwa zikoti zambiri.+
47 Pa nthawiyo kapolo amene anadziwa zofuna za mbuye wake koma osakonzekera kubwera kwake, kapena osachita mogwirizana ndi zofuna za mbuye wakeyo, adzakwapulidwa zikoti zambiri.+