Luka 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Patangopita masiku owerengeka, mwana wamng’ono uja anasonkhanitsa zinthu zonse n’kupita kudziko lina lakutali. Kumeneko anasakaza chuma chake chonse mwa kulowerera m’makhalidwe oipa.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:13 Yesu—Ndi Njira, tsa. 200 Nsanja ya Olonda,10/1/1998, tsa. 92/1/1989, tsa. 8
13 Patangopita masiku owerengeka, mwana wamng’ono uja anasonkhanitsa zinthu zonse n’kupita kudziko lina lakutali. Kumeneko anasakaza chuma chake chonse mwa kulowerera m’makhalidwe oipa.+