Luka 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno mwanayo anauza bambo akewo kuti, ‘Bambo, ndachimwira kumwamba komanso ndachimwira inu.+ Sindilinso woyenera kutchedwa mwana wanu. Munditenge ngati mmodzi wa aganyu anu.’+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:21 Yesu—Ndi Njira, tsa. 202 Nsanja ya Olonda,2/15/1990, tsa. 23
21 Ndiyeno mwanayo anauza bambo akewo kuti, ‘Bambo, ndachimwira kumwamba komanso ndachimwira inu.+ Sindilinso woyenera kutchedwa mwana wanu. Munditenge ngati mmodzi wa aganyu anu.’+