Luka 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Koma mwana wamkulu+ anali kumunda. Ndiyeno pobwerako, atayandikira kunyumbako, anamva anthu akuimba nyimbo ndi kuvina. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:25 Nsanja ya Olonda,2/15/1989, ptsa. 16-17
25 “Koma mwana wamkulu+ anali kumunda. Ndiyeno pobwerako, atayandikira kunyumbako, anamva anthu akuimba nyimbo ndi kuvina.