Luka 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ndionetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa mkazi wamasiyeyu. Ndichita zimenezi kuti asapitirize kumangobwera ndi kundisautsa kwambiri,+ chifukwa mkazi ameneyu akundivutitsa+ mosalekeza.’” Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:5 Nsanja ya Olonda,4/1/2014, tsa. 7
5 ndionetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa mkazi wamasiyeyu. Ndichita zimenezi kuti asapitirize kumangobwera ndi kundisautsa kwambiri,+ chifukwa mkazi ameneyu akundivutitsa+ mosalekeza.’”