Luka 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndithu ndikukuuzani, Iye adzaonetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa iwo mwamsanga.+ Koma, Mwana wa munthu akadzafika, kodi adzapezadi chikhulupiriro padziko lapansi?” Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:8 Yesu—Ndi Njira, tsa. 220 Nsanja ya Olonda,12/15/2006, ptsa. 26-297/1/1989, tsa. 8
8 Ndithu ndikukuuzani, Iye adzaonetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa iwo mwamsanga.+ Koma, Mwana wa munthu akadzafika, kodi adzapezadi chikhulupiriro padziko lapansi?”