Luka 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo anthu anayamba kumubweretsera ana kuti awakhudze ndi manja ake, koma ophunzirawo ataona zimenezo anayamba kuwakalipira.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:15 “Wotsatira Wanga,” tsa. 139 Yesu—Ndi Njira, tsa. 222 Nsanja ya Olonda,7/15/1989, tsa. 9
15 Pamenepo anthu anayamba kumubweretsera ana kuti awakhudze ndi manja ake, koma ophunzirawo ataona zimenezo anayamba kuwakalipira.+