Luka 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwe umadziwa malamulo+ akuti, ‘Usachite chigololo,+ Usaphe munthu,*+ Usabe,+ Usapereke umboni wonama+ ndiponso lakuti, Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako.’”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:20 Nsanja ya Olonda,6/15/1986, ptsa. 8-9
20 Iwe umadziwa malamulo+ akuti, ‘Usachite chigololo,+ Usaphe munthu,*+ Usabe,+ Usapereke umboni wonama+ ndiponso lakuti, Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako.’”+