Luka 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako anatengera pambali ophunzira 12 aja ndi kuwauza kuti: “Tamverani! Tsopano tikupita ku Yerusalemu, ndipo zonse zimene zinalembedwa ndi aneneri,+ zokhudza Mwana wa munthu zikakwaniritsidwa.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:31 Yesu—Ndi Njira, tsa. 228 Nsanja ya Olonda,9/1/1989, tsa. 8
31 Kenako anatengera pambali ophunzira 12 aja ndi kuwauza kuti: “Tamverani! Tsopano tikupita ku Yerusalemu, ndipo zonse zimene zinalembedwa ndi aneneri,+ zokhudza Mwana wa munthu zikakwaniritsidwa.+