Luka 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye anayankha kuti: “Samalani kuti asadzakusocheretseni.+ Pakuti ambiri adzabwera m’dzina langa, n’kumanena kuti, ‘Khristu uja ndine,’ adzanenanso kuti, ‘Nthawi ija yayandikira.’+ Musadzawatsatire.
8 Iye anayankha kuti: “Samalani kuti asadzakusocheretseni.+ Pakuti ambiri adzabwera m’dzina langa, n’kumanena kuti, ‘Khristu uja ndine,’ adzanenanso kuti, ‘Nthawi ija yayandikira.’+ Musadzawatsatire.