Luka 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano tsiku la chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa linafika, tsiku loyenera kupha nyama yoperekera nsembe ya pasika.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:7 Yesu—Ndi Njira, tsa. 267 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 9
7 Tsopano tsiku la chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa linafika, tsiku loyenera kupha nyama yoperekera nsembe ya pasika.+