Luka 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye anawayankha kuti:+ “Mukalowa mumzinda, mwamuna wina wosenza mtsuko wa madzi akumana nanu. Mukamutsatire kunyumba imene akalowe.+
10 Iye anawayankha kuti:+ “Mukalowa mumzinda, mwamuna wina wosenza mtsuko wa madzi akumana nanu. Mukamutsatire kunyumba imene akalowe.+