Luka 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo mukauze mwininyumba imeneyo kuti, ‘Mphunzitsi akufunsa kuti: “Chipinda cha alendo chili kuti, mmene ine ndidyeremo pasika pamodzi ndi ophunzira anga?”’+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:11 Yesu—Ndi Njira, tsa. 267 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 9
11 Ndipo mukauze mwininyumba imeneyo kuti, ‘Mphunzitsi akufunsa kuti: “Chipinda cha alendo chili kuti, mmene ine ndidyeremo pasika pamodzi ndi ophunzira anga?”’+