Luka 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Komabe, inu mwakhalabe ndi ine+ m’mayesero anga.+