Luka 22:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma iye anati: “Ndikukuuza iwe Petulo, Tambala asanalire lero, undikana katatu kuti sundidziwa.”+
34 Koma iye anati: “Ndikukuuza iwe Petulo, Tambala asanalire lero, undikana katatu kuti sundidziwa.”+