Luka 22:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Yesu anauzanso ophunzirawo kuti: “Pamene ndinakutumizani+ opanda chikwama cha ndalama, thumba la chakudya, kapena nsapato, munasowa kanthu kodi?” Iwo anati: “Ayi!”
35 Yesu anauzanso ophunzirawo kuti: “Pamene ndinakutumizani+ opanda chikwama cha ndalama, thumba la chakudya, kapena nsapato, munasowa kanthu kodi?” Iwo anati: “Ayi!”