Luka 22:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pakuti ndikukuuzani kuti mawu olembedwawa ayenera kukwaniritsidwa mwa ine. Mawuwo ndi akuti, ‘Ndipo anamutenga ngati mmodzi wa anthu osamvera malamulo.’+ Pakuti chimene chikukhudza ine chikukwaniritsidwa.”+
37 Pakuti ndikukuuzani kuti mawu olembedwawa ayenera kukwaniritsidwa mwa ine. Mawuwo ndi akuti, ‘Ndipo anamutenga ngati mmodzi wa anthu osamvera malamulo.’+ Pakuti chimene chikukhudza ine chikukwaniritsidwa.”+