Luka 22:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Mawu adakali m’kamwa, panafika khamu la anthu, limodzi ndi Yudasi, mmodzi wa ophunzira 12 aja, akuwatsogolera.+ Ndiyeno Yudasi anapita pamene panali Yesu kukamupsompsona.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:47 Yesu—Ndi Njira, tsa. 284 Nsanja ya Olonda,10/15/1990, tsa. 8
47 Mawu adakali m’kamwa, panafika khamu la anthu, limodzi ndi Yudasi, mmodzi wa ophunzira 12 aja, akuwatsogolera.+ Ndiyeno Yudasi anapita pamene panali Yesu kukamupsompsona.+