Luka 22:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Koma Yesu anati: “Basi! Lekani zimenezi.” Ndipo anagwira khutu lija ndi kumuchiritsa.+