Luka 22:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Atasonkha moto mkati mwa bwalo ndi kukhala pansi onse pamodzi, Petulo nayenso anakhala nawo pamenepo.+
55 Atasonkha moto mkati mwa bwalo ndi kukhala pansi onse pamodzi, Petulo nayenso anakhala nawo pamenepo.+