Luka 22:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Koma mayi wina wantchito anamuona atakhala pafupi ndi moto wowala ndipo anamuyang’ana ndi kunena kuti: “Bambo awanso anali naye limodzi.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:56 Yesu—Ndi Njira, tsa. 288
56 Koma mayi wina wantchito anamuona atakhala pafupi ndi moto wowala ndipo anamuyang’ana ndi kunena kuti: “Bambo awanso anali naye limodzi.”+