Luka 22:66 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Kenako kutacha, bungwe la akulu, kuphatikizapo ansembe aakulu komanso alembi, anasonkhana pamodzi,+ ndipo anamutengera kuholo ya Khoti Lalikulu la Ayuda.* Kumeneko iwo anati:+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:66 Yesu—Ndi Njira, tsa. 290 Nsanja ya Olonda,12/1/1990, tsa. 8
66 Kenako kutacha, bungwe la akulu, kuphatikizapo ansembe aakulu komanso alembi, anasonkhana pamodzi,+ ndipo anamutengera kuholo ya Khoti Lalikulu la Ayuda.* Kumeneko iwo anati:+