Luka 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamenepo khamu lonselo linanyamuka, onse pamodzi, n’kupita naye kwa Pilato.+