Luka 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndi kuwauza kuti: “Inu mwabweretsa munthu uyu kwa ine monga wolimbikitsa anthu kuukira. Koma mwaona nokha pano! Inetu ndamufunsa pamaso panu, ndipo sindinamupeze ndi chifukwa+ chomuimbira milandu imene mukumunenezayi.
14 ndi kuwauza kuti: “Inu mwabweretsa munthu uyu kwa ine monga wolimbikitsa anthu kuukira. Koma mwaona nokha pano! Inetu ndamufunsa pamaso panu, ndipo sindinamupeze ndi chifukwa+ chomuimbira milandu imene mukumunenezayi.