Luka 23:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Munthu ameneyu sanavomereze chiwembu chawo ndi zochita zawo.+ Yosefe anali wochokera ku Arimateya, mzinda wa Ayudeya, ndipo anali kuyembekezera ufumu wa Mulungu.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:51 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2017, ptsa. 18-19 Nsanja ya Olonda,10/15/1990, tsa. 14
51 Munthu ameneyu sanavomereze chiwembu chawo ndi zochita zawo.+ Yosefe anali wochokera ku Arimateya, mzinda wa Ayudeya, ndipo anali kuyembekezera ufumu wa Mulungu.+