-
Luka 24:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Amayiwo anagwidwa ndi mantha ndi kuweramira pansi. Ndiyeno amunawo anawafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani mukufunafuna Munthu wamoyo pakati pa akufa?
-