Luka 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Paja ananena kuti Mwana wa munthu ayenera kuperekedwa m’manja mwa anthu ochimwa ndi kupachikidwa, ndi kuuka tsiku lachitatu.”+
7 Paja ananena kuti Mwana wa munthu ayenera kuperekedwa m’manja mwa anthu ochimwa ndi kupachikidwa, ndi kuuka tsiku lachitatu.”+