Luka 24:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ataona izi, maso awo anatsegukiratu ndipo anamuzindikira, kenako iye anazimiririka.+