Luka 24:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Onani manja ndi mapazi angawa, mutsimikize kuti ndine ndithu. Ndikhudzeni muone,+ chifukwa mzimu ulibe mnofu ndi mafupa+ ngati anga amene mukuwaonawa.” Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:39 Kukambitsirana, ptsa. 108-109
39 Onani manja ndi mapazi angawa, mutsimikize kuti ndine ndithu. Ndikhudzeni muone,+ chifukwa mzimu ulibe mnofu ndi mafupa+ ngati anga amene mukuwaonawa.”