Yohane 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iyeyu anabwera kwa Yesu usiku+ ndi kumuuza kuti: “Rabi,+ tikudziwa kuti inu ndinu mphunzitsi+ wochokera kwa Mulungu,+ chifukwa munthu sangathe kuchita zizindikiro+ zimene inu mumachita ngati Mulungu sali naye.”+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:2 Muzikonda Anthu, lesson 10 Nsanja ya Olonda,2/1/2002, ptsa. 9-11
2 Iyeyu anabwera kwa Yesu usiku+ ndi kumuuza kuti: “Rabi,+ tikudziwa kuti inu ndinu mphunzitsi+ wochokera kwa Mulungu,+ chifukwa munthu sangathe kuchita zizindikiro+ zimene inu mumachita ngati Mulungu sali naye.”+