Yohane 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho anatolera zonse, ndipo zinadzaza madengu 12 kuchokera pa mitanda ya mkate wa balere isanu ija, imene onse anadya ndi kuilephera.+
13 Choncho anatolera zonse, ndipo zinadzaza madengu 12 kuchokera pa mitanda ya mkate wa balere isanu ija, imene onse anadya ndi kuilephera.+