-
Yohane 6:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Iwo anakwera ngalawa ndi kuyamba kuwoloka nyanja kulowera ku Kaperenao. Pa nthawiyi n’kuti mdima utagwa ndipo Yesu anali asanabwerebe kwa iwo.
-