Yohane 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yesu anawayankha kuti: “Ndithudi ndikukuuzani, Mukundifunafuna osati chifukwa munaona zizindikiro ayi, koma chifukwa munadya mikate ndi kukhuta.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:26 Nsanja ya Olonda,11/15/1987, tsa. 6
26 Yesu anawayankha kuti: “Ndithudi ndikukuuzani, Mukundifunafuna osati chifukwa munaona zizindikiro ayi, koma chifukwa munadya mikate ndi kukhuta.+