Yohane 6:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Pamenepo Ayudawo anayamba kung’ung’udza za iye chifukwa ananena kuti: “Ine ndine chakudya chotsika kumwamba.”+
41 Pamenepo Ayudawo anayamba kung’ung’udza za iye chifukwa ananena kuti: “Ine ndine chakudya chotsika kumwamba.”+