Yohane 6:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Iwo anayamba kunena kuti:+ “Kodi uyu si Yesu mwana wa Yosefe,+ amene bambo ake ndi mayi ake tikuwadziwa? Nanga bwanji pano akunena kuti, ‘Ndinatsika kumwamba’?”
42 Iwo anayamba kunena kuti:+ “Kodi uyu si Yesu mwana wa Yosefe,+ amene bambo ake ndi mayi ake tikuwadziwa? Nanga bwanji pano akunena kuti, ‘Ndinatsika kumwamba’?”