Yohane 6:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Koma Yesuyo, pakuti anadziwa payekha kuti ophunzira ake akung’ung’udza pa mawuwo, anafunsa kuti: “Kodi mawuwa mwakhumudwa+ nawo?
61 Koma Yesuyo, pakuti anadziwa payekha kuti ophunzira ake akung’ung’udza pa mawuwo, anafunsa kuti: “Kodi mawuwa mwakhumudwa+ nawo?