Yohane 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamenepo Ayudawo anayamba kunena kuti: “Kodi akufuna kudzipha? Nanga n’chifukwa chiyani akunena kuti, ‘Kumene ine ndikupita inu simungathe kukafikako?’”+
22 Pamenepo Ayudawo anayamba kunena kuti: “Kodi akufuna kudzipha? Nanga n’chifukwa chiyani akunena kuti, ‘Kumene ine ndikupita inu simungathe kukafikako?’”+