Yohane 8:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Zimene ndinaziona kwa Atate wanga+ ndi zimene ndimalankhula.+ Chotero inunso mumachita zimene mwamva kwa atate wanu.” Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:38 Yesu—Ndi Njira, tsa. 164 Nsanja ya Olonda,5/15/1988, tsa. 8
38 Zimene ndinaziona kwa Atate wanga+ ndi zimene ndimalankhula.+ Chotero inunso mumachita zimene mwamva kwa atate wanu.”