Yohane 8:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Ayudawo anati: “Tsopano tadziwa ndithu kuti uli ndi chiwanda.+ Abulahamu anamwalira,+ ndiponso aneneri.+ Koma iwe ukunena kuti, ‘Ngati munthu asunga mawu anga sadzalawa+ imfa.’
52 Ayudawo anati: “Tsopano tadziwa ndithu kuti uli ndi chiwanda.+ Abulahamu anamwalira,+ ndiponso aneneri.+ Koma iwe ukunena kuti, ‘Ngati munthu asunga mawu anga sadzalawa+ imfa.’