Yohane 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Onse amene abwera m’malo mwa ine ndi akuba ndiponso ofunkha,+ ndipo nkhosa sizinawamvere.+