Yohane 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ine ndine khomo.+ Aliyense wolowa kudzera mwa ine adzapulumuka, ndipo azidzalowa ndi kutuluka, kukapeza msipu.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:9 Yesu—Ndi Njira, tsa. 186
9 Ine ndine khomo.+ Aliyense wolowa kudzera mwa ine adzapulumuka, ndipo azidzalowa ndi kutuluka, kukapeza msipu.+