Yohane 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho Ayuda anamuzungulira ndi kuyamba kumuuza kuti: “Utivutitsa maganizo mpaka liti? Ngati ndiwedi Khristu,+ tiuze mosapita m’mbali.”+
24 Choncho Ayuda anamuzungulira ndi kuyamba kumuuza kuti: “Utivutitsa maganizo mpaka liti? Ngati ndiwedi Khristu,+ tiuze mosapita m’mbali.”+