Yohane 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kutangotsala masiku 6 kuti pasika ayambike, Yesu anafika ku Betaniya+ kumene kunali Lazaro,+ uja amene Yesu anamuukitsa kwa akufa. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:1 Yesu—Ndi Njira, tsa. 236 Nsanja ya Olonda,10/15/1989, tsa. 82/15/1986, tsa. 32
12 Kutangotsala masiku 6 kuti pasika ayambike, Yesu anafika ku Betaniya+ kumene kunali Lazaro,+ uja amene Yesu anamuukitsa kwa akufa.