Yohane 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ana apamtima inu,+ ndikhala nanu kanthawi kochepa chabe. Mudzandifunafuna, ndipo monga ndinauzira Ayuda aja kuti, ‘Kumene ine ndikupita simungathe kukafikako,’+ tsopano ndikuuzanso inuyo. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:33 Nsanja ya Olonda,2/1/2003, tsa. 13
33 Ana apamtima inu,+ ndikhala nanu kanthawi kochepa chabe. Mudzandifunafuna, ndipo monga ndinauzira Ayuda aja kuti, ‘Kumene ine ndikupita simungathe kukafikako,’+ tsopano ndikuuzanso inuyo.